Ekisodo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ine ndikudziwa bwino kuti mfumu ya Iguputo sidzakulolani kupita kufikira nditaisonyeza mphamvu zanga.+ Ekisodo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+
19 Koma ine ndikudziwa bwino kuti mfumu ya Iguputo sidzakulolani kupita kufikira nditaisonyeza mphamvu zanga.+
3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+