2 Mafumu 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+ Yobu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi Wamphamvuyonse ndani kuti tim’tumikire?+Ndipo kulankhula naye kungatipindulitse chiyani?’+ Aroma 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chakuti, ngakhale anam’dziwa Mulungu, iwo sanam’patse ulemerero monga Mulungu kapena kumuyamikira.+ M’malomwake anayamba kulingalira zinthu zopanda pake+ ndipo mtima wawo wopusawo unachita mdima.+
35 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+
21 Chifukwa chakuti, ngakhale anam’dziwa Mulungu, iwo sanam’patse ulemerero monga Mulungu kapena kumuyamikira.+ M’malomwake anayamba kulingalira zinthu zopanda pake+ ndipo mtima wawo wopusawo unachita mdima.+