Ekisodo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+ Salimo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kutukumuka mtima kwake, woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.+Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+ Hoseya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+
2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+
4 Chifukwa cha kutukumuka mtima kwake, woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.+Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+
6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+