Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 35:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,

      Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+

  • Salimo 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana ana a anthu padziko lapansi,+

      Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, aliyense amene akufunafuna Yehova.+

  • Yeremiya 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iwo sananene kuti, ‘Ali kuti Yehova, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo,+ amene anatitsogolera m’chipululu,+ m’dera lam’chipululu lodzaza ndi mayenje, m’dziko lopanda madzi+ ndi la mdima wandiweyani,+ dziko limene simunadutse munthu aliyense komanso mmene simunali kukhala munthu aliyense?’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena