Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 51:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi n’chifukwa chiyani ukuiwala Yehova amene anakupanga,+ amene anatambasula kumwamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi?+ N’chifukwa chiyani ukuchita mantha nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu, poopa mkwiyo wa yemwe akukupanikizira mkati,+ ngati kuti iye wakonzeka kuti akuwononge?+ Kodi mkwiyo wa amene akukupanikizira mkati uli kuti?+

  • 1 Petulo 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+

  • Chivumbulutso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena