Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+

  • 2 Mbiri 36:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.

  • Esitere 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha.

  • Salimo 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kusakaza kwa mdani kwatheratu tsopano,+

      Mizinda imene mwaifafaniza, nayonso yatheratu.+

      Dzina la mdani wanu silidzatchulidwanso.+

  • Yesaya 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chotero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ wanena kuti: “Anthu anga amene mukukhala m’Ziyoni,+ musachite mantha chifukwa cha Msuri amene anali kukukwapulani ndi chikwapu+ ndiponso kukumenyani ndi ndodo, ngati mmene Iguputo anali kuchitira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena