Ekisodo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ponena za ana a Isiraeli, Farao adzati, ‘Asokonezeka ndipo akungoyendayenda m’dziko lathu. Chipululu chawatsekera.’+ Ekisodo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Motero Aiguputo anali kuwathamangira, ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi+ ndi magulu ake ankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa m’mphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyang’anizana ndi Baala-zefoni.+
3 Ndiyeno ponena za ana a Isiraeli, Farao adzati, ‘Asokonezeka ndipo akungoyendayenda m’dziko lathu. Chipululu chawatsekera.’+
9 Motero Aiguputo anali kuwathamangira, ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi+ ndi magulu ake ankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa m’mphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyang’anizana ndi Baala-zefoni.+