Salimo 71:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo akunena kuti: “Mulungu wamusiya.+Mulondoleni ndi kumugwira pakuti palibe womulanditsa.”+