Salimo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ponena za moyo wanga, ambiri akuti:“Mulungu sam’pulumutsa ameneyu.”+ [Seʹlah.*] Salimo 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Odana nane akunditonza kwambiri moti zikungokhala ngati mafupa anga aphwanyidwa,+Pakuti anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Mateyu 27:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+
10 Odana nane akunditonza kwambiri moti zikungokhala ngati mafupa anga aphwanyidwa,+Pakuti anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+