2 Samueli 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wakubwezera mlandu wonse wa magazi a nyumba ya Sauli amene iwe unamulowa m’malo monga mfumu. Yehova wapereka ufumu m’manja mwa Abisalomu mwana wako. Ndipo tsopano tsoka lakugwera chifukwa uli ndi mlandu wamagazi!”+ Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Mateyu 27:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+
8 Yehova wakubwezera mlandu wonse wa magazi a nyumba ya Sauli amene iwe unamulowa m’malo monga mfumu. Yehova wapereka ufumu m’manja mwa Abisalomu mwana wako. Ndipo tsopano tsoka lakugwera chifukwa uli ndi mlandu wamagazi!”+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+