Salimo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ponena za moyo wanga, ambiri akuti:“Mulungu sam’pulumutsa ameneyu.”+ [Seʹlah.*] Salimo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Anadzipereka kwa Yehova.+ Amupulumutse Iyeyo!+Ngati Mulungu amamukonda, amulanditse!”+ Salimo 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Odana nane akunditonza kwambiri moti zikungokhala ngati mafupa anga aphwanyidwa,+Pakuti anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
10 Odana nane akunditonza kwambiri moti zikungokhala ngati mafupa anga aphwanyidwa,+Pakuti anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+