Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ponena za moyo wanga, ambiri akuti:

      “Mulungu sam’pulumutsa ameneyu.”+ [Seʹlah.*]

  • Salimo 79:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+

      Pamene mukubwezera anthu a mitundu inawo chifukwa cha magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa,+

      Ife tidzaone ndi maso athu.+

  • Yoweli 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Ansembe ndi atumiki a Yehova alire m’khonde mwa guwa lansembe+ ndipo anene kuti, ‘Inu Yehova, mverani chisoni anthu anu ndipo musachititse manyazi cholowa chanu+ kuti mitundu ya anthu iwalamulire. Anthu a mitundu ina asanene kuti: “Kodi Mulungu wawo ali kuti?”’+

  • Mika 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mdani wanga adzaona zimenezi, ndipo amene anali kunena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ adzachita manyazi.+ Maso anga adzamuyang’ana.+ Iye adzakhala malo opondedwapondedwa ngati matope a mumsewu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena