Yeremiya 51:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mkazi wokhala mu Ziyoni adzanena kuti, ‘Chiwawa chimene achitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Yerusalemu adzanena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu okhala m’dziko la Kasidi.’”+ Aroma 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+ Chivumbulutso 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+
35 Mkazi wokhala mu Ziyoni adzanena kuti, ‘Chiwawa chimene achitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Yerusalemu adzanena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu okhala m’dziko la Kasidi.’”+
19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+
20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+