Mateyu 27:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+ Luka 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu anangoima chilili kuonerera zochitikazo.+ Koma olamulira anali kumunyogodola kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, m’lekeni adzipulumutse yekha,+ ngati iyeyu alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+
43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+
35 Anthu anangoima chilili kuonerera zochitikazo.+ Koma olamulira anali kumunyogodola kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, m’lekeni adzipulumutse yekha,+ ngati iyeyu alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+