Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 14:62
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Pamenepo Yesu anati: “Inde ndinedi, ndipo anthu inu mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+

  • Yohane 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pa chifukwa chimenechi, Ayudawo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, anali kunenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana+ ndi Mulungu.

  • Yohane 10:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena