Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa chifukwa chimenechi Ayudawo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere, chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, ankanenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana ndi Mulungu.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Kukambitsirana, ptsa. 428-429 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 19
18 Pa chifukwa chimenechi Ayudawo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere, chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, ankanenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana ndi Mulungu.+