Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+ Salimo 102:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lonse adani anga amanditonza.+Anthu ondinyoza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.+
11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+
8 Tsiku lonse adani anga amanditonza.+Anthu ondinyoza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.+