Salimo 102:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lonse adani anga amandinyoza.+ Anthu amene amanditonza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.
8 Tsiku lonse adani anga amandinyoza.+ Anthu amene amanditonza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.