Salimo 102:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lonse adani anga amanditonza.+Anthu ondinyoza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.+
8 Tsiku lonse adani anga amanditonza.+Anthu ondinyoza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.+