Salimo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Maso anga achita mdima chifukwa cha chisoni changa.+Maso anga akalamba chifukwa cha anthu onse ondichitira zoipa.+ Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+ Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+ Luka 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+
7 Maso anga achita mdima chifukwa cha chisoni changa.+Maso anga akalamba chifukwa cha anthu onse ondichitira zoipa.+
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+
9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+