Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+ Luka 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Yohane 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+
9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+
21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+