Yohane 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+ Machitidwe 7:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+ Machitidwe 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo m’bale wake wa Yohane+ anamupha ndi lupanga.+ Chivumbulutso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera,+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pang’ono, kufikira chitakwanira chiwerengero cha akapolo anzawo, ndi abale awo amene anali pafupi kuphedwa+ monga mmene iwonso anaphedwera.
2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+
59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+
11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera,+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pang’ono, kufikira chitakwanira chiwerengero cha akapolo anzawo, ndi abale awo amene anali pafupi kuphedwa+ monga mmene iwonso anaphedwera.