Mateyu 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anawauza kuti: “Inde mudzamwadi+ zimene ndatsala pang’ono kumwa. Koma kunena zokhala kudzanja langa lamanja ndi lamanzere, si ine wopereka mwayi umenewo, koma Atate wanga adzaupereka kwa amene anawakonzera.”+ Luka 11:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pa nkhani imeneyi, nzeru+ ya Mulungu inanenanso kuti, ‘Ndidzawatumizira aneneri ndi atumwi, koma iwo adzapha ndi kuzunza ena mwa iwo.
23 Iye anawauza kuti: “Inde mudzamwadi+ zimene ndatsala pang’ono kumwa. Koma kunena zokhala kudzanja langa lamanja ndi lamanzere, si ine wopereka mwayi umenewo, koma Atate wanga adzaupereka kwa amene anawakonzera.”+
49 Pa nkhani imeneyi, nzeru+ ya Mulungu inanenanso kuti, ‘Ndidzawatumizira aneneri ndi atumwi, koma iwo adzapha ndi kuzunza ena mwa iwo.