Mateyu 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anawauza kuti: “Inde mudzamwadi zimene ndatsala pangʼono kumwa.+ Koma si ine woyenera kusankha amene adzakhale kudzanja langa lamanja kapena lamanzere. Atate wanga adzapereka mwayi umenewo kwa amene anawakonzera.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:23 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 14 Kukambitsirana, tsa. 396
23 Iye anawauza kuti: “Inde mudzamwadi zimene ndatsala pangʼono kumwa.+ Koma si ine woyenera kusankha amene adzakhale kudzanja langa lamanja kapena lamanzere. Atate wanga adzapereka mwayi umenewo kwa amene anawakonzera.”+