Mateyu 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anawauza kuti: “Inde mudzamwadi+ zimene ndatsala pang’ono kumwa. Koma kunena zokhala kudzanja langa lamanja ndi lamanzere, si ine wopereka mwayi umenewo, koma Atate wanga adzaupereka kwa amene anawakonzera.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:23 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 14 Kukambitsirana, tsa. 396
23 Iye anawauza kuti: “Inde mudzamwadi+ zimene ndatsala pang’ono kumwa. Koma kunena zokhala kudzanja langa lamanja ndi lamanzere, si ine wopereka mwayi umenewo, koma Atate wanga adzaupereka kwa amene anawakonzera.”+