Yohane 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu adzakuchotsani musunagoge.+ Ndipotu nthawi ikubwera pamene aliyense amene adzakupheni+ adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 278 Nsanja ya Olonda,9/1/1990, tsa. 8
2 Anthu adzakuchotsani musunagoge.+ Ndipotu nthawi ikubwera pamene aliyense amene adzakupheni+ adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.