Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako anthu adzakuperekani kuti mukazunzidwe+ ndipo adzakuphani.+ Anthu a mitundu yonse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+

  • Machitidwe 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Saulo anavomereza zoti Sitefano aphedwe.+

      Tsiku limenelo, mpingo umene unali ku Yerusalemu unayamba kuzunzidwa koopsa. Choncho ophunzira onse, kupatula atumwi okha, anabalalika nʼkupita mʼzigawo za Yudeya ndi Samariya.+

  • Machitidwe 12:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawi imeneyi Mfumu Herode* anayamba kuzunza anthu ena amumpingo.+ 2 Iye anapha ndi lupanga+ Yakobo, mchimwene wake wa Yohane.+

  • Machitidwe 26:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nthawi zambiri ndinkawapatsa chilango mʼmasunagoge onse, pofuna kuwakakamiza kuti asiye zimene amakhulupirira. Popeza ndinali nditakwiya nawo kwambiri, ndinafika powazunza ngakhale mʼmizinda yakunja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena