Yohane 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzikumbukira mawu amene ndinakuuzani aja: Kapolo sangakhale wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso mawu anu. Machitidwe 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amene anabalalika+ chifukwa cha mavuto amene anayamba chifukwa cha zimene zinachitikira Sitefano, anakafika mpaka ku Foinike, ku Kupuro ndi ku Antiokeya. Ndipo ankangolalikira kwa Ayuda okha.+ Chivumbulutso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi apitiriza kuponya mʼndende ena a inu kuti muyesedwe mpaka pamapeto, ndipo mudzakhala mʼmasautso kwa masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+
20 Muzikumbukira mawu amene ndinakuuzani aja: Kapolo sangakhale wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso mawu anu.
19 Anthu amene anabalalika+ chifukwa cha mavuto amene anayamba chifukwa cha zimene zinachitikira Sitefano, anakafika mpaka ku Foinike, ku Kupuro ndi ku Antiokeya. Ndipo ankangolalikira kwa Ayuda okha.+
10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi apitiriza kuponya mʼndende ena a inu kuti muyesedwe mpaka pamapeto, ndipo mudzakhala mʼmasautso kwa masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+