Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu adzakuchotsani musunagoge.+ Ndipotu nthawi ikubwera pamene aliyense amene adzakupheni+ adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.

  • Machitidwe 7:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.”

  • Machitidwe 12:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawi imeneyi Mfumu Herode* anayamba kuzunza anthu ena amumpingo.+ 2 Iye anapha ndi lupanga+ Yakobo, mchimwene wake wa Yohane.+

  • Chivumbulutso 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pangʼono, mpaka chiwerengero cha akapolo anzawo chitakwanira, inde chiwerengero cha abale awo amene anali atatsala pangʼono kuphedwa ngati mmenenso iwowo anaphedwera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena