Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+ Maliko 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Koma amene adzapirire mpaka pa mapeto,+ ndiye amene adzapulumuke.+
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+
13 Ndipo anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Koma amene adzapirire mpaka pa mapeto,+ ndiye amene adzapulumuke.+