Yobu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha kuzunzika, diso langa layamba kuchita mdima.+Ziwalo zanga zonse zakhala ngati mthunzi. Salimo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+
7 Chifukwa cha kuzunzika, diso langa layamba kuchita mdima.+Ziwalo zanga zonse zakhala ngati mthunzi.
9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+