Salimo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka. Salimo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndathiridwa pansi ngati madzi.+Mafupa anga onse alekanalekana.+Mtima wanga wakhala ngati phula,+Wasungunuka mkati mwanga.+
2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka.
14 Ndathiridwa pansi ngati madzi.+Mafupa anga onse alekanalekana.+Mtima wanga wakhala ngati phula,+Wasungunuka mkati mwanga.+