Deuteronomo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno atsogoleri apitirize kulankhula ndi anthuwo kuti, ‘Kodi pali wamantha ndi wosalimba mtima?+ Achoke ndi kubwerera kunyumba yake, kuti angachititse mantha mitima ya abale ake ngati mmene wachitira mtima wake.’+ Mateyu 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+ Maliko 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Popita kumeneko anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane,+ ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika kwambiri mumtima mwake.+
8 Ndiyeno atsogoleri apitirize kulankhula ndi anthuwo kuti, ‘Kodi pali wamantha ndi wosalimba mtima?+ Achoke ndi kubwerera kunyumba yake, kuti angachititse mantha mitima ya abale ake ngati mmene wachitira mtima wake.’+
38 Kenako anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+
33 Popita kumeneko anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane,+ ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika kwambiri mumtima mwake.+