Oweruza 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano lengeza ndipo anthu onse amve, kuti, ‘Alipo kodi akuchita mantha ndi kunjenjemera? Abwerere.’”+ Choncho ndi mawu amenewa, Gidiyoni anayesa anthuwo. Pamenepo, anthu 22,000 anabwerera ndipo panatsala anthu 10,000.
3 Tsopano lengeza ndipo anthu onse amve, kuti, ‘Alipo kodi akuchita mantha ndi kunjenjemera? Abwerere.’”+ Choncho ndi mawu amenewa, Gidiyoni anayesa anthuwo. Pamenepo, anthu 22,000 anabwerera ndipo panatsala anthu 10,000.