Salimo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani adani anga achuluka chotere?+N’chifukwa chiyani anthu ondiukira achuluka?+ Salimo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ponena za moyo wanga, ambiri akuti:“Mulungu sam’pulumutsa ameneyu.”+ [Seʹlah.*] Salimo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova Mulungu wanga,+ ine ndathawira kwa inu.+Ndipulumutseni kwa onse ondizunza ndipo mundilanditse,+ Salimo 71:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo akunena kuti: “Mulungu wamusiya.+Mulondoleni ndi kumugwira pakuti palibe womulanditsa.”+
3 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani adani anga achuluka chotere?+N’chifukwa chiyani anthu ondiukira achuluka?+
7 Inu Yehova Mulungu wanga,+ ine ndathawira kwa inu.+Ndipulumutseni kwa onse ondizunza ndipo mundilanditse,+ Salimo 71:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo akunena kuti: “Mulungu wamusiya.+Mulondoleni ndi kumugwira pakuti palibe womulanditsa.”+