Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+ Salimo 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+