Salimo 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani. N’chifukwa chiyani mukugonabe, inu Yehova?+Dzukani. Musatitaye kwamuyaya.+