Salimo 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Dzukani. Nʼchifukwa chiyani mukugonabe, inu Yehova?+ Dzukani. Musatitaye kwamuyaya.+