Yobu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chiyani mukubisa nkhope yanu,+Nʼkumandiona ngati mdani wanu?+ Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala mpaka liti, inu Yehova? Mpaka kalekale? Kodi mudzandibisira nkhope yanu mpaka liti?+ Salimo 88:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, nʼchifukwa chiyani mukundikana?+ Nʼchifukwa chiyani mukundibisira nkhope yanu?+
13 Kodi mudzandiiwala mpaka liti, inu Yehova? Mpaka kalekale? Kodi mudzandibisira nkhope yanu mpaka liti?+