Yobu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chiyani mukubisa nkhope yanu,+N’kunditenga ine ngati mdani wanu?+ Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+ Salimo 88:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani mukunditaya?+N’chifukwa chiyani mukundibisira nkhope yanu?+
13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+