Salimo 88:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, nʼchifukwa chiyani mukundikana?+ Nʼchifukwa chiyani mukundibisira nkhope yanu?+