Salimo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Moyo wanga wasokonezeka kwambiri.+Kodi inu Yehova, mudzadikira kufikira liti?+ Salimo 88:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani mukunditaya?+N’chifukwa chiyani mukundibisira nkhope yanu?+ Yesaya 59:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+
2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+