Salimo 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+
2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+