Salimo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+ Salimo 140:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa,+ mpulumutsi wanga wamphamvu,+Mwatchinga ndi kuteteza mutu wanga pa tsiku lankhondo.+
7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+
7 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa,+ mpulumutsi wanga wamphamvu,+Mwatchinga ndi kuteteza mutu wanga pa tsiku lankhondo.+