Salimo 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+
9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+