Salimo 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndasokonezeka ndipo ndawerama kwambiri chifukwa cha chisoni changa.+Ndayenda uku ndi uku tsiku lonse ndili wachisoni.+ Salimo 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+ Mlaliki 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinaganiziranso kuponderezana+ konse kumene kukuchitika padziko lapansi pano, ndipo ndinaona misozi ya anthu amene akuponderezedwa,+ koma panalibe wowatonthoza.+ M’manja mwa oponderezawo munali mphamvu, moti oponderezedwawo analibe wowatonthoza.
6 Ndasokonezeka ndipo ndawerama kwambiri chifukwa cha chisoni changa.+Ndayenda uku ndi uku tsiku lonse ndili wachisoni.+
2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+
4 Ine ndinaganiziranso kuponderezana+ konse kumene kukuchitika padziko lapansi pano, ndipo ndinaona misozi ya anthu amene akuponderezedwa,+ koma panalibe wowatonthoza.+ M’manja mwa oponderezawo munali mphamvu, moti oponderezedwawo analibe wowatonthoza.