Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 35:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chifukwa cha kuchuluka kwa kuponderezedwa, iwo amangokhalira kufuula popempha thandizo.+

      Amangokhalira kulirira thandizo chifukwa cha dzanja la amphamvu.+

  • Amosi 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’

  • Mika 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena