17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+
11 Chonde, lero abwezereni minda yawo ya tirigu,+ minda yawo ya mpesa, minda yawo ya maolivi, nyumba zawo ndi limodzi mwa magawo 100 a ndalama, tirigu, vinyo watsopano ndi mafuta zimene munalandira kwa iwo monga chiwongoladzanja.”