Genesis 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Poyankha, Abulamu anauza Sarai+ kuti: “Kapolo wakoyutu ali m’manja mwako. Chita chimene ukuchiona kuti n’chabwino.”+ Pamenepo Sarai anayamba kuzunza Hagara, mpaka Hagarayo anathawa kwa Sarai.+
6 Poyankha, Abulamu anauza Sarai+ kuti: “Kapolo wakoyutu ali m’manja mwako. Chita chimene ukuchiona kuti n’chabwino.”+ Pamenepo Sarai anayamba kuzunza Hagara, mpaka Hagarayo anathawa kwa Sarai.+