Miyambo 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wonyoza amadana ndi munthu amene akum’dzudzula.+ Iye sadzapita kwa anthu anzeru.+ Mlaliki 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu wa mtsogoleri ukakuukira, usachoke pamalo ako,+ chifukwa kudekha kumachepetsa machimo aakulu.+ 1 Petulo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi kupirira kumenyedwa mbama mutachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma ngati mukupirira povutika chifukwa cha kuchita zabwino,+ zimenezo n’zabwino kwa Mulungu.+
4 Mzimu wa mtsogoleri ukakuukira, usachoke pamalo ako,+ chifukwa kudekha kumachepetsa machimo aakulu.+
20 Kodi kupirira kumenyedwa mbama mutachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma ngati mukupirira povutika chifukwa cha kuchita zabwino,+ zimenezo n’zabwino kwa Mulungu.+